Genesis 42:31 - Buku Lopatulika Koma ife tinati kwa iye, Tili anthu oona; sitili ozonda; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma ife tinati kwa iye, Tili anthu oona; sitili ozonda; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ife tidamuuza munthuyo kuti, ‘Ndife anthu okhulupirika, osati azondi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma tinamuwuza kuti, ‘Ndife anthu woona mtima osati akazitape. |
tili abale khumi ndi awiri, ana a atate wathu; wina palibe, ndipo lero wamng'ono ali ndi atate wathu m'dziko la Kanani.