anaitana aamuna a m'nyumba yake, nanena ndi iwo kuti, Taonani, walowetsa kwa ife Muhebri kuti atiseke ife, analowa kwa ine kugona ndi ine, ndipo ndinafuula ndi mau aakulu:
Genesis 39:15 - Buku Lopatulika ndipo panali pamene iye anamva kuti ndinakweza mau anga ndi kufuula, iye anasiya chofunda chake kwa ine nathawira kubwalo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo panali pamene iye anamva kuti ndinakweza mau anga ndi kufuula, iye anasiya chofunda chake kwa ine nathawira kubwalo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono atamva kukuwa kwangako, wasiya mwinjiro wake m'manja mwangamu nkuthaŵira pabwalo.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atandimva ndikukuwa, anandisiyira mkanjo wakewu nʼkuthawira kunja.” |
anaitana aamuna a m'nyumba yake, nanena ndi iwo kuti, Taonani, walowetsa kwa ife Muhebri kuti atiseke ife, analowa kwa ine kugona ndi ine, ndipo ndinafuula ndi mau aakulu:
Afunafuna zosalungama; kusanthula, asanthuladi mpaka kutha; chingakhale cha m'kati mwake mwa munthu, ndi mtima wozama.