Genesis 38:27 - Buku Lopatulika Ndipo panali nthawi ya kubala kwake, taonani, amapasa anali m'mimba mwake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo panali nthawi ya kubala kwake, taonani, amapasa anali m'mimba mwake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Itakwana nthaŵi yakuti Tamara achire, m'mimba mwake munali mapasa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamene Tamara nthawi inamukwanira yoti abeleke, mʼmimbamo munali mapasa. |
Ndipo panali pamene anabala kuti mmodzi anatulutsa dzanja; ndipo namwino anatenga chingwe chofiira namanga padzanja lake, kuti, Uyu anayamba kubadwa.