Genesis 38:13 - Buku Lopatulika Ndipo anamuuza Tamara, kuti, Taona, mpongozi wako akwera kunka ku Timna kuti akasenge nkhosa zake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anamuuza Tamara, kuti, Taona, mpongozi wako akwera kunka ku Timna kuti akasenge nkhosa zake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Munthu wina adauza Tamara kuti, “Apongozi ako akupita ku Timna kukameta nkhosa.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tamara atamva kuti apongozi ake akupita ku Timna kukameta nkhosa, |
Ndi Tamara mpongozi wake anambalira Perezi ndi Zera. Ana aamuna onse a Yuda ndiwo asanu.
Ndipo malire anazungulira kuyambira ku Baala kunka kumadzulo, kuphiri la Seiri, napitirira kumbali kwa phiri la Yearimu kumpoto, ndilo Kesaloni, natsikira ku Betesemesi, napitirira ku Timna;
Ndipo panali munthu ku Maoni, amene katundu wake anali ku Karimele; iyeyu anali womveka ndithu, anali nazo nkhosa zikwi zitatu, ndi mbuzi chikwi chimodzi; ndipo analikusenga nkhosa zake ku Karimele.