Ndipo anampeza munthu, taonani, analinkusokera m'thengo; munthuyo ndipo anamfunsa, nati, Kodi ufuna chiyani?
Genesis 37:16 - Buku Lopatulika Ndipo iye anati, Ndifuna abale anga. Undiuzetu kumene adyetsa zoweta. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo iye anati, Ndifuna abale anga. Undiuzetu kumene adyetsa zoweta. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Ndikufunafuna abale anga. Chonde tandiwuzani kumene akuŵeta nkhosa.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iye anayankha, “Ndikufuna abale anga. Mungandiwuze kumene akudyetsa ziweto zawo?” |
Ndipo anampeza munthu, taonani, analinkusokera m'thengo; munthuyo ndipo anamfunsa, nati, Kodi ufuna chiyani?
Munthuyo ndipo anati, Anachoka pano; pakuti ndinamva alinkuti, Timuke ku Dotani. Yosefe ndipo anatsata abale ake, nawapeza ali ku Dotani.
Ndiuze, iwe amene moyo wanga ukukonda, umaweta kuti gulu lako? Umaligonetsa kuti pakati pa usana? Pakuti ndikhalirenji ngati wosochera pambali pa magulu a anzako?