Landiranitu mdalitso wanga umene wafika kwa inu, pakuti Mulungu wandichitira ine zaufulu, ndipo zanganso zindikwanira. Ndipo anamkakamiza, nalandira.
Genesis 33:12 - Buku Lopatulika Ndipo Esau anati, Tiyeni timuke; nditsogolera ndine. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Esau anati, Tiyeni timuke; nditsogolera ndine. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndipo Esau adati, “Tiyeni tinyamuke, tizipita. Ine nditsogolako.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Esau anati, “Tiyeni tizipita; nditsagana nanu.” |
Landiranitu mdalitso wanga umene wafika kwa inu, pakuti Mulungu wandichitira ine zaufulu, ndipo zanganso zindikwanira. Ndipo anamkakamiza, nalandira.
Ndipo anati kwa iye, Mbuyanga adziwa kuti ana ali anthete, ndipo nkhosa ndi zoweta ndili nazo zilinkuyamwitsa: ndipo akathamangitsa tsiku limodzi zoweta zonse zidzafa.