mbuzi zazikazi mazana awiri, atonde makumi awiri, nkhosa zazikazi mazana awiri, ndi zazimuna makumi awiri,
Genesis 32:15 - Buku Lopatulika ngamira zamkaka makumi atatu ndi ana ao, ng'ombe zazikazi makumi anai, zazimuna khumi, abulu aakazi makumi awiri ndi ana khumi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ngamira zamkaka makumi atatu ndi ana ao, ng'ombe zazikazi makumi anai, zazimuna khumi, abulu akazi makumi awiri ndi ana khumi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ngamira zamkaka makumi atatu pamodzi ndi ana ake, ng'ombe zazikazi makumi anai, ndi zazimuna khumi, ndi abulu aakazi makumi aŵiri ndi amphongo khumi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ngamira za mkaka 30 ndi ana awo, ngʼombe zazikazi 40 ndi zazimuna khumi, ndipo abulu aakazi makumi awiri ndi abulu aamuna khumi. |
mbuzi zazikazi mazana awiri, atonde makumi awiri, nkhosa zazikazi mazana awiri, ndi zazimuna makumi awiri,
Ndipo anazipereka zimenezo m'manja a anyamata ake, gulu pa lokha gulu pa lokha: ndipo anati kwa anyamata ake, Taolokani patsogolo panga, tachitani danga pakati pa magulu, lina ndi lina.