koma udzanke kunyumba ya atate wanga, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga mkazi.
Genesis 24:39 - Buku Lopatulika Ndipo ndinati kwa mbuyanga, Kapena mkazi sadzanditsata ine. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ndinati kwa mbuyanga, Kapena mkazi sadzanditsata ine. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndipo ine ndidamuyankha mbuyanga kuti, ‘Nanga zidzatani ngati mkaziyo adzakana kubwera nane kuno?’ Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Ndipo ine ndinati kwa mbuye wanga, ‘Nanga mkaziyo akakapanda kubwera nane pamodzi?’ |
koma udzanke kunyumba ya atate wanga, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga mkazi.
Ndipo anati kwa iye mnyamatayo, Kapena sadzafuna mkaziyo kunditsata ine ku dziko lino: kodi ndikambwezerenso mwana wanu ku dziko komwe mwachokera inu?