Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Genesis 24:18 - Buku Lopatulika

Ndipo anati, Imwa mbuyanga; nafulumira nayangata mtsuko m'manja mwake namwetsa iye.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Ndipo anati, Imwa mbuyanga; nafulumira nayangata mtsuko m'manja mwake namwetsa iye.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Namwaliyo adati, “Imwani mbuyanga,” ndipo mosachedwa adatsitsa mtsuko wake uja pa phewa, naugwirira kuti mlendoyo amwe.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Mtsikanayo anati, “Imwani mbuye wanga.” Ndipo mofulumira anatsitsa mtsuko uja nawuyika mʼmanja ndi kumupatsa kuti amwe.

Onani mutuwo



Genesis 24:18
6 Mawu Ofanana  

ndipo pakhale kuti namwali amene ndidzati kwa iye, Tulatu mtsuko wako, ndimwe; ndipo iye adzati, Imwa, ndipo ndidzamwetsanso ngamira zako; yemweyo akhale mkazi wosankhira mnyamata wanu Isaki; ndipo chotero ndidzadziwa kuti mwamchitira mbuyanga ufulu.


Ndipo iye anafulumira, natsitsa mtsuko pa phewa lake, nati, Imwatu, ndipo ndidzamwetsanso ngamira zako: ndipo ndinamwa, ndipo anamwetsa ngamira.


Ndipo m'mene analikumuka kukatenga iye anamuitananso, nati, Unditengerenso kanthongo ka mkate m'dzanja lako.


Atsegula pakamwa pake ndi nzeru, ndipo chilangizo cha chifundo chili pa lilime lake.


Chotsalira, khalani nonse a mtima umodzi, ochitirana chifundo, okondana ndi abale, achisoni, odzichepetsa;