Genesis 23:5 - Buku Lopatulika Ndipo ana a Hiti anayankha Abrahamu nati kwa iye, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ana a Hiti anayankha Abrahamu nati kwa iye, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthuwo adamuyankha kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthu a ku Hiti aja anamuyankha Abrahamu kuti, |
Ine ndine mlendo wakukhala ndi inu: mundipatse ndikhale ndi manda pamodzi ndi inu, kuti ndiike wakufa wanga ndisamthirenso maso.
Mutimvere ife mfumu, ndinu kalonga wamkulu pakati pa ife; muike wakufa wanu m'manda mwathu mosankhika: palibe munthu yense wa ife adzakaniza manda ake, kuti muike wakufa wanu.