Ndipo ananena kwa Efuroni alinkumva anthu a m'dzikomo, kuti, Koma ngati ufuna, undimveretu ine: ndidzakupatsa iwe mtengo wake wa munda; uulandire kwa ine, ndipo ndidzaika wakufa wanga m'menemo.
Genesis 23:14 - Buku Lopatulika Ndipo Efuroni anamyankha Abrahamu, nati kwa iye, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Efuroni anamyankha Abrahamu, nati kwa iye, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma Efuroni adayankha kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma Efroni anamuyankha Abrahamu nati, |
Ndipo ananena kwa Efuroni alinkumva anthu a m'dzikomo, kuti, Koma ngati ufuna, undimveretu ine: ndidzakupatsa iwe mtengo wake wa munda; uulandire kwa ine, ndipo ndidzaika wakufa wanga m'menemo.
Mfumu, mundimvere ine; kadziko ka mtengo wake wa masekeli a siliva mazana anai, ndiko chiyani pakati pa ine ndi inu? Ikani wakufa wanu.