Ndipo Farao anaitana Abramu, nati, Nanga nchiyani ichi wandichitira ine? Chifukwa chanji sunandiuze ine kuti ndiye mkazi wako?
Genesis 20:10 - Buku Lopatulika Ndipo Abimeleki anati kwa Abrahamu, Unaona chiyani iwe kuti wachita ichi? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Abimeleki anati kwa Abrahamu, Unaona chiyani iwe kuti wachita ichi? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chifukwa chiyani wachita zimenezi?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Abrahamu anafunsa Abimeleki kuti, “Chifukwa chiyani wachita zimenezi?” |
Ndipo Farao anaitana Abramu, nati, Nanga nchiyani ichi wandichitira ine? Chifukwa chanji sunandiuze ine kuti ndiye mkazi wako?
Ndipo Abrahamu anati, Chifukwa ndinati, Pompano palibe ndithu kumuopa Mulungu, ndipo adzandipha ine chifukwa cha mkazi wanga.
Ndipo Abimeleki anaitana Abrahamu, nati kwa iye, Watichitira ife chiyani iwe? Ndakuchimwiranji iwe kuti waufikitsa pa ine ndi pa ufumu wanga uchimo waukulu? Wandichitira ine zosayenera kuzichita.