Fulumira, thawira kumeneko; pakuti sindithai kuchita kanthu usadafike kumeneko. Chifukwa chake anatcha dzina la mzindawo Zowari.
Genesis 19:23 - Buku Lopatulika Ndipo dzuwa lidakwera padziko pamene Loti anafika ku Zowari. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo dzuwa lidakwera pa dziko pamene Loti anafika ku Zowari. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene dzuŵa linkatuluka, Loti nkuti atafika kale ku Zowari. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamene Loti amafika ku Zowari, nʼkuti dzuwa litatuluka. |
Fulumira, thawira kumeneko; pakuti sindithai kuchita kanthu usadafike kumeneko. Chifukwa chake anatcha dzina la mzindawo Zowari.
Ndipo Yehova anavumbitsa pa Sodomu ndi pa Gomora miyala ya sulufure ndi moto kutuluka kwa Mulungu kumwamba;
Ndipo kudamchera iye pamene anaoloka pa Penuwele, ndipo iye anatsimphina ndi ntchafu yake.