Ndipo Hagara anambalira Abramu mwana wamwamuna ndipo Abramu anatcha dzina la mwana wake amene anambalira iye Hagara, Ismaele.
Genesis 17:25 - Buku Lopatulika Ndipo Ismaele mwana wake anali wa zaka khumi ndi zitatu pamene anadulidwa m'khungu lake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Ismaele mwana wake anali wa zaka khumi ndi zitatu pamene anadulidwa m'khungu lake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mwana wake Ismaele anali wa zaka 13 pamene adaumbalidwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndipo mwana wake Ismaeli anali ndi zaka khumi ndi zitatu; |
Ndipo Hagara anambalira Abramu mwana wamwamuna ndipo Abramu anatcha dzina la mwana wake amene anambalira iye Hagara, Ismaele.
Ndipo Abramu anali wa zaka makumi asanu ndi atatu kudza zisanu ndi chimodzi, pamene Hagara anambalira Abramu Ismaele.