ndipo Reu anakhala ndi moyo zaka mazana awiri kudza zisanu ndi ziwiri, atabala Serugi, nabala ana aamuna ndi aakazi.
Genesis 11:22 - Buku Lopatulika Ndipo Serugi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Nahori: Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Serugi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Nahori: Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Serugi ali wa zaka 30, adabereka mwana dzina lake Nahori. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamene Serugi anali ndi zaka makumi atatu, anabereka Nahori. |
ndipo Reu anakhala ndi moyo zaka mazana awiri kudza zisanu ndi ziwiri, atabala Serugi, nabala ana aamuna ndi aakazi.
ndipo Serugi anakhala ndi moyo zaka mazana awiri, atabala Nahori, nabala ana aamuna ndi aakazi.
Ndipo Yoswa ananena ndi anthu onse, Atero Yehova Mulungu wa Israele, Kale lija makolo anu anakhala tsidya lija la mtsinje, ndiye Tera, atate wa Abrahamu ndi atate wa Nahori; natumikira milungu ina iwowa.