ndipo Pelegi anakhala ndi moyo zaka mazana awiri kudza zisanu ndi zinai, atabala Reu, nabala ana aamuna ndi aakazi.
Genesis 11:20 - Buku Lopatulika Ndipo Reu anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza ziwiri, nabala Serugi: Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Reu anakhala ndi moyo zaka makumi atatu kudza ziwiri, nabala Serugi: Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Reu ali wa zaka 32, adabereka mwana dzina lake Serugi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamene Reu anali ndi zaka 32, anabereka Serugi. |
ndipo Pelegi anakhala ndi moyo zaka mazana awiri kudza zisanu ndi zinai, atabala Reu, nabala ana aamuna ndi aakazi.
ndipo Reu anakhala ndi moyo zaka mazana awiri kudza zisanu ndi ziwiri, atabala Serugi, nabala ana aamuna ndi aakazi.
Ndipo amenewo anatuluka usana. Koma Benihadadi analinkumwa naledzera m'misasamo, iye ndi mafumu aja makumi atatu mphambu awiri aja akumthandiza.
Ndipo anthu anafikira zikwi khumi ndi zisanu ndi chimodzi; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo anthu makumi atatu mphambu awiri.