ndipo Eberi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza makumi awiri, atabala Pelegi, nabala ana aamuna ndi aakazi.
Genesis 11:18 - Buku Lopatulika Ndipo Pelegi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Reu; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Pelegi anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Reu; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pelegi ali wa zaka 30 adabereka mwana dzina lake Reu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamene Pelegi anali ndi zaka makumi atatu, anabereka Reu. |
ndipo Eberi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza makumi awiri, atabala Pelegi, nabala ana aamuna ndi aakazi.
ndipo Pelegi anakhala ndi moyo zaka mazana awiri kudza zisanu ndi zinai, atabala Reu, nabala ana aamuna ndi aakazi.