ndipo Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza zitatu, atabala Sela, nabala ana aamuna ndi aakazi.
Genesis 11:14 - Buku Lopatulika Ndipo Sela anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Eberi; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Sela anakhala ndi moyo zaka makumi atatu, nabala Eberi; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene Sela anali wa zaka 30, adabereka mwana dzina lake Eberi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamene Sela anali ndi zaka makumi atatu, anabereka Eberi. |
ndipo Aripakisadi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza zitatu, atabala Sela, nabala ana aamuna ndi aakazi.
ndipo Sela anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza zitatu, atabala Eberi, nabala ana aamuna ndi aakazi.