Genesis 10:28 - Buku Lopatulika ndi Obala, ndi Abimaele, ndi Sheba; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi Obala, ndi Abimaele, ndi Sheba; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Obala, Abimaele, Sheba, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Obali, Abimaeli, Seba, |
Ndipo Yokisani anabala Sheba, ndi Dedani. Ana a Dedani ndi Aasuri, ndi Aletusi, ndi Aleumi.
Ndipo atamva mfumu yaikazi ya ku Sheba mbiri ya Solomoni yakubukitsa dzina la Yehova, anadza kumuyesera iye ndi miyambi yododometsa.
Harani ndi Kane ndi Edeni, amalonda a ku Sheba Asiriya ndi Kilimadi, anagulana nawe malonda.