Kwa Eberi ndipo kunabadwa ana aamuna awiri; dzina la wina ndi Pelegi; chifukwa kuti m'masiku ake dziko lapansi linagawanikana; dzina la mphwake ndi Yokotani.
Genesis 10:26 - Buku Lopatulika Ndipo Yokotani anabala Alimodadi, ndi Selefi, ndi Hazara-Maveti, ndi Yera; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yokotani anabala Alimodadi, ndi Selefi, ndi Hazara-Maveti, ndi Yera; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yokotani adabereka Alimodadi, Selefi, Hazara-Maveti, Yera, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yokitani anabereka Alimodadi, Selefi, Hazari-Maveti, Yera, |
Kwa Eberi ndipo kunabadwa ana aamuna awiri; dzina la wina ndi Pelegi; chifukwa kuti m'masiku ake dziko lapansi linagawanikana; dzina la mphwake ndi Yokotani.