Ndipo akapitao a ana a Israele anaona kuti kudawaipira, pamene ananena, Musamachepetsa njerwa zanu, ntchito ya tsiku pa tsiku lake.
Eksodo 5:20 - Buku Lopatulika Ndipo potuluka kwa Farao iwo anakomana ndi Mose ndi Aroni, alikuima popenyana nao; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo potuluka kwa Farao iwo anakomana ndi Mose ndi Aroni, alikuima popenyana nao; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono atachoka kwa Farao kuja, adakumana ndi Mose ndi Aroni amene ankaŵadikira, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atachoka pamaso pa Farao, anakumana ndi Mose ndi Aaroni akuwadikira, |
Ndipo akapitao a ana a Israele anaona kuti kudawaipira, pamene ananena, Musamachepetsa njerwa zanu, ntchito ya tsiku pa tsiku lake.
ndipo ananena nao, Yehova akupenyeni, naweruze; pakuti mwatinyansitsa pamaso pa Farao, ndi pamaso pa anyamata ake, ndi kuwapatsa lupanga m'dzanja lao kutipha nalo.