Nyengo zanga zili m'manja mwanu, mundilanditse m'manja a adani anga, ndi kwa iwo akundilondola ine.
Eksodo 40:37 - Buku Lopatulika koma ukapanda kukwera mtambo, samayenda ulendo wao kufikira tsiku loti wakwera. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 koma ukapanda kukwera mtambo, samayenda ulendo wao kufikira tsiku loti wakwera. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma mtambowo ukapanda kuchoka, Aisraele sankachokanso pachigonopo. Ankadikira tsiku lakuti mtambo wachokapo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma ngati mtambo sunachoke, iwo sankasamukanso mpaka tsiku limene udzachoke. |
Nyengo zanga zili m'manja mwanu, mundilanditse m'manja a adani anga, ndi kwa iwo akundilondola ine.