Eksodo 37:27 - Buku Lopatulika Ndipo analipangira mphete ziwiri zagolide pansi pa mkombero wake, pangodya zake ziwiri, pa mbali zake ziwiri, zikhale zopisamo mphiko kulinyamulira nazo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo analipangira mphete ziwiri zagolide pansi pa mkombero wake, pangodya zake ziwiri, pa mbali zake ziwiri, zikhale zopisamo mphiko kulinyamulira nazo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adapanga mphete ziŵiri zagolide zonyamulira guwalo, ndipo adazilumikiza ku mbali zonse ziŵiri za guwa, pansi pa mkombero uja, kuti apisemo mphiko zonyamulira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anapanga mphete ziwiri pansi pa mkomberowo ndi kulumikiza ku mbali zonse ziwiri kuti apisemo nsichi zonyamulira. |
Ndipo analikuta ndi golide woona, pamwamba pake, ndi mbali zake pozungulira, ndi nyanga zake; ndipo analipangira mkombero wagolide pozungulira pake.