Eksodo 36:32 - Buku Lopatulika ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali inzake ya chihema, ndi mitanda isanu ya matabwa a chihema ali pa mbali ya kumadzulo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali inzake ya Kachisi, ndi mitanda isanu ya matabwa a Kachisi ali pa mbali ya kumadzulo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa isanu ya mafulemu a mbali inayo, ndiponso isanu ya mafulemu a mbali yakuzambwe, kumbuyo kwake kwa chihema. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero mitanda isanu inanso inali ya maferemu a mbali inayo ndipo mitanda ina isanu ya mbali yakumadzulo, kumapeto kwenikweni kwa chihema. |