Ndi ku mbali ina ya chihema, mbali ya kumpoto, anapanga matabwa makumi awiri, ndi makamwa ao makumi anai asiliva;
Eksodo 36:26 - Buku Lopatulika makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ndi masinde ake makumi anai asiliva, masinde aŵiri pansi pa fulemu lililonse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndiponso matsinde makumi anayi asiliva, awiri pansi pa feremu iliyonse. |
Ndi ku mbali ina ya chihema, mbali ya kumpoto, anapanga matabwa makumi awiri, ndi makamwa ao makumi anai asiliva;