napanga makamwa makumi anai asiliva pansi pa matabwa makumi awiri; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi kwa mitsukwa yake iwiri, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina kwa mitsukwa yake iwiri.
Eksodo 36:25 - Buku Lopatulika Ndi ku mbali ina ya chihema, mbali ya kumpoto, anapanga matabwa makumi awiri, ndi makamwa ao makumi anai asiliva; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi ku mbali ina ya Kachisi, mbali ya kumpoto, anapanga matabwa makumi awiri, ndi makamwa ao makumi anai asiliva; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pa mbali yakumpoto ya chihemacho adapanganso mafulemu makumi aŵiri Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iwo anapanganso maferemu makumi awiri a mbali yakumpoto ya chihemacho, |
napanga makamwa makumi anai asiliva pansi pa matabwa makumi awiri; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi kwa mitsukwa yake iwiri, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina kwa mitsukwa yake iwiri.