Pa thabwa limodzi panakhala mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; anawapanga momwemo matabwa onse a chihema.
Eksodo 36:23 - Buku Lopatulika Ndipo anapanga matabwa a chihema; matabwa makumi awiri a ku mbali ya kumwera, kumwera; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anapanga matabwa a Kachisi; matabwa makumi awiri a ku mbali ya kumwera, kumwera; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pa mbali yakumwera adapanga mafulemu makumi aŵiri, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anapanga maferemu makumi awiri a mbali yakummwera kwa chihemacho, |
Pa thabwa limodzi panakhala mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; anawapanga momwemo matabwa onse a chihema.
napanga makamwa makumi anai asiliva pansi pa matabwa makumi awiri; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi kwa mitsukwa yake iwiri, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina kwa mitsukwa yake iwiri.