Pa thabwa limodzi pakhale mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; uzitero pa matabwa onse a chihema.
Eksodo 36:22 - Buku Lopatulika Pa thabwa limodzi panakhala mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; anawapanga momwemo matabwa onse a chihema. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pa thabwa limodzi panakhala mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; anawapanga momwemo matabwa onse a Kachisi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Thabwa lililonse linali ndi zolumikizira ziŵiri, ndipo mafulemu onse adaŵapanga ndi zolumikizira ziŵiri. Mafulemu onse adaŵapanga ndi zolumikizira zotere. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Thabwa lililonse linali ndi zolumikizira ziwiri. Iwo anapanga maferemu onse a chihemacho ndi matabwa otere. |
Pa thabwa limodzi pakhale mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; uzitero pa matabwa onse a chihema.
Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwa limodzi ndiko mkono ndi hafu.