Eksodo 36:21 - Buku Lopatulika Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwa limodzi ndiko mkono ndi hafu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Utali wake wa thabwa limodzi ndiwo mikono khumi, ndi kupingasa kwake kwa thabwa limodzi ndiko mkono ndi hafu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'litali mwa fulemu lililonse munali mamita anai ndi theka, ndipo muufupi mwake munali masentimita 69. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Feremu iliyonse inali yotalika mamita anayi ndipo mulifupi mwake munali masentimita 69. |
Pa thabwa limodzi panakhala mitsukwa iwiri, yomangika pamodzi; anawapanga momwemo matabwa onse a chihema.