Utali wake wa nsalu imodzi ndiwo mikono makumi atatu, ndi kupingasa kwake kwa nsalu imodzi ndiko mikono inai; nsalu khumi ndi imodzi zinafanana muyeso wao.
Eksodo 36:14 - Buku Lopatulika Ndipo anaomba nsalu zophimba za ubweya wa mbuzi zikhale chophimba pamwamba pa chihema; anaomba nsalu zophimba khumi ndi imodzi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anaomba nsalu zophimba za ubweya wa mbuzi zikhale hema pamwamba pa Kachisi; anaomba nsalu zophimba khumi ndi imodzi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pambuyo pake adasoka nsalu khumi ndi imodzi za ubweya wambuzi, napanga chophimbira pamwamba pa chihemacho. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iwo anapanga nsalu za ubweya wambuzi zophimba pamwamba pa chihemacho. Nsalu zonse pamodzi zinalipo khumi ndi imodzi. |
Utali wake wa nsalu imodzi ndiwo mikono makumi atatu, ndi kupingasa kwake kwa nsalu imodzi ndiko mikono inai; nsalu khumi ndi imodzi zinafanana muyeso wao.