ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wakasiya;
Eksodo 35:9 - Buku Lopatulika ndi miyala yasohamu, ndi miyala yoika ya efodi, ndi ya chapachifuwa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi miyala yasohamu, ndi miyala yoika ya efodi, ndi ya chapachifuwa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa miyala ya mtundu wa onikisi ndi ina yokoma yoika pa chovala chaunsembe cha efodi ndiponso pa chovala chapachifuwa.’ ” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero miyala yokongola ya mtundu wa onikisi ndi ina yabwino yoyika pa Efodi ndi pa chovala cha pachifuwa. |
ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wakasiya;
ndi mafuta akuunikira, ndi zonunkhira za mafuta odzoza, ndi chofukiza cha fungo lokoma;