Ndipo uziomba nsalu zophimba za ubweya wa mbuzi zikhale chophimba pamwamba pa chihema; uziomba nsalu khumi ndi imodzi.
Eksodo 35:12 - Buku Lopatulika likasa, ndi mphiko zake, chotetezerapo, ndi nsalu yotchinga yotseka; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 likasa, ndi mphiko zake, chotetezerapo, ndi nsalu yotchinga yotseka; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Apangenso bokosi lachipangano ndi mphiko zake, chivundikiro chake cha bokosilo ndi nsalu zotchinga bokosilo; Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Bokosi la Chipangano pamodzi ndi mitengo yake yonyamulira ndiponso chovundikira chake cha bokosilo ndi nsalu zophimba bokosilo; |
Ndipo uziomba nsalu zophimba za ubweya wa mbuzi zikhale chophimba pamwamba pa chihema; uziomba nsalu khumi ndi imodzi.