Ndipo ulankhule ndi onse a mtima waluso, amene ndawadzaza ndi mzimu waluso, kuti amsokere Aroni zovala apatulidwe nazo, andichitire Ine ntchito ya nsembe.
Eksodo 35:10 - Buku Lopatulika Ndipo abwere yense wa mtima waluso mwa inu, napange zonse zimene Yehova analamula; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo abwere yense wa mtima waluso mwa inu, napange zonse zimene Yehova anauza; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Anthu onse aluso pakati panupa abwere, ndipo apange zonse zimene Chauta adalamula. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Anthu onse aluso pakati panu abwere ndi kupanga zonse zimene Yehova walamula: |
Ndipo ulankhule ndi onse a mtima waluso, amene ndawadzaza ndi mzimu waluso, kuti amsokere Aroni zovala apatulidwe nazo, andichitire Ine ntchito ya nsembe.
Potero anatsiriza ntchito yonse ya Kachisi wa chihema chokomanako; ndipo ana a Israele adachita monga mwa zonse Yehova adamuuza Mose, anachita momwemo.