Eksodo 35:1 - Buku Lopatulika Ndipo Mose anasonkhanitsa khamu lonse la ana a Israele, nanena nao, Siwa mau amene Yehova analamula, kuti muwachite. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Mose anasonkhanitsa khamu lonse la ana a Israele, nanena nao, Siwa mau amene Yehova anauza, kuti muwachite. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mose adaitana Aisraele onse naŵauza kuti, “Chauta akukulamulani kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mose anasonkhanitsa gulu lonse la Aisraeli ndipo anawawuza kuti, “Zinthu zimene Yehova wakulamulirani kuti muzichite ndi izi: |
Ndipo atatero, ana onse a Israele anayandikiza; ndipo iye anawauza zonse Yehova adalankhula naye m'phiri la Sinai.
pakuti akumvaimva lamulo sakhala olungama pamaso pa Mulungu, koma akuchita lamulo adzayesedwa olungama.