Guwa la nsembe lomwe lamkuwa, adalipanga Bezalele mwana wa Uri mwana wa Huri linali komweko, ku khomo la chihema cha Yehova; ndipo Solomoni ndi khamulo anafunako.
Eksodo 31:9 - Buku Lopatulika ndi guwa la nsembe yopsereza ndi zipangizo zake zonse, ndi mkhate ndi tsinde lake; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi guwa la nsembe yopsereza ndi zipangizo zake zonse, ndi mkhate ndi tsinde lake; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa guwa la zopereka zopsereza, pamodzi ndi zipangizo zake, beseni losambira ndi phaka lake, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero guwa lansembe yopsereza ndi ziwiya zake zonse, beseni ndi nsichi yake, |
Guwa la nsembe lomwe lamkuwa, adalipanga Bezalele mwana wa Uri mwana wa Huri linali komweko, ku khomo la chihema cha Yehova; ndipo Solomoni ndi khamulo anafunako.