Eksodo 30:27 - Buku Lopatulika ndi guwalo ndi zipangizo zake zonse, ndi choikaponyali ndi zipangizo zake, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi gomelo ndi zipangizo zake zonse, ndi choikapo nyali ndi zipangizo zake, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa tebulo ndi zipangizo zake zonse, choikaponyale pamodzi ndi zida zake, guwa lofukizirapo lubani, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero tebulo, ndi ziwiya zake zonse, choyikapo nyale ndi zipangizo zake, guwa lofukizirapo lubani, |
ndi guwa la nsembe lofukizapo, ndi guwa la nsembe yopsereza ndi zipangizo zake zonse, ndi mkhate wosambiramo ndi tsinde lake.
Kapena sayatsa nyali, ndi kuivundikira m'mbiya, koma aiika iyo pa choikapo chake; ndipo iunikira onse ali m'nyumbamo.