ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ina ya chihema, ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ya chihema cha kumbuyo kumadzulo.
Eksodo 26:28 - Buku Lopatulika Ndi mtanda wa pakati pa matabwa ufikire kuthungo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi mtanda wa pakati pa matabwa ufikire kuthungo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mtanda wa pakati penipeni pa mafulemuwo ugwire mafulemu onse, kuyambira ku mapeto mpaka ku mapeto. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mtanda wapakati pa maferemuwo uchokere pa maferemu a mbali ina mpaka mbali inanso. |
ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ina ya chihema, ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali ya chihema cha kumbuyo kumadzulo.
Ndipo uzikuta matabwa ndi golide, ndi kupanga mphete zao zagolide zopisamo mitandayo; uzikutanso mitandayo ndi golide.