Achipange ichi ndi zipangizo izi zonse za talente wa golide woona.
Choikaponyalecho ndi zipangizo zonse uzipange ndi golide wolemera makilogaramu 34.
Choyikapo nyale ndi zipangizo zonse zipangidwe ndi golide wabwino kwambiri wolemera makilogalamu 34.
Ndipo mbano zake, ndi zoolera zake, zikhale za golide woona.
Ndipo uyang'anire uzipanga monga mwachifaniziro chao, chimene anakuonetsa m'phirimo.