Eksodo 25:32 - Buku Lopatulika ndipo m'mbali zake mutuluke mphanda zisanu ndi imodzi; mphanda zitatu za choikaponyalicho zituluke m'mbali yake ina, ndi mphanda zitatu za choikaponyalicho zituluke m'mbali inzake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo m'mbali zake mutuluke mphanda zisanu ndi imodzi; mphanda zitatu za choikapo nyalicho zituluke m'mbali yake ina, ndi mphanda zitatu za choikapo nyalicho zituluke m'mbali inzake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pa mbali zake pakhale mphanda zisanu ndi imodzi, zitatu pa mbali iliyonse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mʼmbali mwake mukhale mphanda zisanu ndi imodzi, zitatu mbali iliyonse. |
ndi m'mbali zake munatuluka mphanda zisanu ndi imodzi; mphanda zitatu za choikaponyali zotuluka m'mbali yake imodzi, ndi mphanda zitatu za choikaponyali zotuluka m'mbali yake ina;
Kapena sayatsa nyali, ndi kuivundikira m'mbiya, koma aiika iyo pa choikapo chake; ndipo iunikira onse ali m'nyumbamo.