Ndipo ulikute ndi golide woona, ulikute m'kati ndi kubwalo, nulipangire mkombero wagolide pozungulira pake.
Eksodo 25:24 - Buku Lopatulika Ndipo ulikute ndi golide woona ndi kulipangira mkombero wagolide pozungulira pake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ulikute ndi golide woona ndi kulipangira mkombero wagolide pozungulira pake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono ulikute ndi golide wabwino kwambiri ndipo pozungulira pake ponse upange mkombero wagolide. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tebulolo ulikute ndi golide wabwino kwambiri ndipo upange mkombero wagolide mʼmbali mwake. |
Ndipo ulikute ndi golide woona, ulikute m'kati ndi kubwalo, nulipangire mkombero wagolide pozungulira pake.
Nulipangire mitanda pozungulirapo yoyesa chikhato m'kupingasa kwake, ndi pamitanda pake pozungulira upangirepo mkombero wagolide.
Ndipo ulikute ndi golide woona, pamwamba pake ndi mbali zake zozungulira, ndi nyanga zake; ulipangirenso mkombero wagolide pozungulira.
Ndipo utiike m'mizere iwiri, tisanu ndi kamodzi mzere umodzi, pa gome loyera, pamaso pa Yehova.