Ndipo mphikozo zinatalika kuti nsonga za mphiko zidaoneka ku malo opatulika chakuno cha chipinda chamkati; koma sizinaoneke kubwalo; ndipo zikhala pomwepo mpaka lero lino.
Eksodo 25:15 - Buku Lopatulika Mphiko zikhale m'zimphete za likasa; asazisolole. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mphiko zikhale m'zimphete za likasa; asazisolole. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mphikozo zidzangokhala m'mphetezo osazitulutsanso. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Nsichizo zizikhala mʼmphete za bokosilo nthawi zonse, zisamachotsedwe. |
Ndipo mphikozo zinatalika kuti nsonga za mphiko zidaoneka ku malo opatulika chakuno cha chipinda chamkati; koma sizinaoneke kubwalo; ndipo zikhala pomwepo mpaka lero lino.
Ndipo zinatalikitsa mphikozo, kuti nsonga za mphiko zidaoneka kulikasa chakuno cha chipinda chamkati, koma sizinaoneke kubwalo; ndipo zili komweko mpaka lero lino.