Eksodo 21:33 - Buku Lopatulika Munthu akafukula dzenje, kapena akakumba dzenje, osalivundikira, ndipo ikagwamo ng'ombe kapena bulu, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Munthu akafukula dzenje, kapena akakumba dzenje, osalivundikira, ndipo ikagwamo ng'ombe kapena bulu, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Munthu akasiya dzenje lapululu, kapena akakumba dzenje, koma osaphimbira, tsono ng'ombe kapena bulu nkugweramo, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Munthu akasiya dzenje lapululu kapena akakumba dzenje koma wosaphimbapo, ndipo ngʼombe kapena bulu nʼkugweramo, |
Ng'ombeyo ikatunga mnyamata kapena mdzakazi, azipatsa mbuye wake ndalama za masekeli a siliva makumi atatu, ndipo ng'ombeyo aiponye miyala.
Wosocheretsa oongoka mtima alowe m'njira yoipa, adzagwa mwini m'dzenje lake; koma angwiro adzalandira cholowa chabwino.
Kodi choipa chibwezedwe pa chabwino? Pakuti akumbira moyo wanga dzenje. Mukumbukire kuti ndinaima pamaso panu kuwanenera zabwino, kuwachotsera iwo ukali wanu.
Mfuu umvekedwe m'nyumba zao, pamene muwatengera khamu la nkhondo dzidzidzi; pakuti akumba dzenje lakundigwira ine, anabisira mapazi anga misampha.