Akolose 3:21 - Buku Lopatulika Atate inu, musaputa ana anu, kuti angataye mtima. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Atate inu, musaputa ana anu, kuti angataye mtima. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inu atate, musamaŵapsetsa mtima ana anu, kuti angataye mtima. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Inu abambo, musakwiyitse ana anu, kuti angataye mtima. |
Ndipo atate inu, musakwiyitse ana anu; komatu muwalere iwo m'maleredwe ndi chilangizo cha Ambuye.
Akapolo inu, mverani m'zonse iwo amene ali ambuye monga mwa thupi, wosati ukapolo wa pamaso, monga okondweretsa anthu, komatu ndi mtima wakulinga kumodzi, akuopa Ambuye;
monga mudziwa kuti tinachitira yense wa inu pa yekha, monga atate achitira ana ake a iye yekha,