Koma Yohane anati amkanize, nanena, Ndiyenera ine kubatizidwa ndi Inu, ndipo Inu mudza kwa ine kodi?
Ahebri 7:23 - Buku Lopatulika Ndipo iwo ndiwo ambiri anakhala ansembe, popeza imfa idawaletsa asakhalebe; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo iwo ndiwo ambiri anakhala ansembe, popeza imfa idawaletsa asakhalebe; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kusiyana kwina nkwakuti ansembe akale aja anali ambiri, chifukwa ankafa, sankatha kupitirira ndi udindo waowo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tsono ansembe akale aja analipo ambiri, popeza imfa imawalepheretsa kupitiriza ntchitoyi. |
Koma Yohane anati amkanize, nanena, Ndiyenera ine kubatizidwa ndi Inu, ndipo Inu mudza kwa ine kodi?
koma Iye ndi lumbiro mwa Iye amene anenana kwa Iye, Walumbira Ambuye ndipo sadzalapa, iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha).
Ndipo pano anthu ofeka alandira limodzi la magawo khumi; koma apo iye, woti adamchitira umboni kuti ali ndi moyo.