Ahebri 4:5 - Buku Lopatulika Ndipo m'menemonso, Ngati adzalowa mpumulo wanga. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo m'menemonso, Ngati adzalowa mpumulo wanga. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Panonso akunena za zomwezo pamene akuti, “Sadzaloŵa konse mu mpumulo umene ndidaŵakonzera.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pa ndime inonso akunena za zomwezo pamene akuti, “Iwo sadzalowa konse mu mpumulo wanga.” |
Popeza ife amene takhulupirira tilowa mpumulowo, monga momwe ananena, Monga ndalumbira mu mkwiyo wanga, ngati adzalowa mpumulo wanga. Zingakhale ntchitozo zidatsirizika kuyambira kuzika kwa dziko lapansi.