Koma undikonzerenso pogona; pakuti ndiyembekeza kuti mwa mapemphero anu ndidzapatsidwa kwa inu.
Ahebri 13:19 - Buku Lopatulika Ndipo ndikudandaulirani koposa kuchita ichi, kuti kubwera kwanga kwa inu kufulumidwe. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ndikudandaulirani koposa kuchita ichi, kuti kubwera kwanga kwa inu kufulumidwe. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndikukupemphani makamaka kuti mupemphere kuti Mulungu andibwezere kwa inu msanga. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ine ndikukupemphani kuti mundipempherere kuti Mulungu andibwezere kwa inu msanga. |
Koma undikonzerenso pogona; pakuti ndiyembekeza kuti mwa mapemphero anu ndidzapatsidwa kwa inu.
Koma ndidandaulira inu, abale, lolani mau a chidandauliro; pakutinso ndalembera inu mwachidule.