Ahebri 10:18 - Buku Lopatulika Koma pomwe pali chikhululukiro cha machimo palibenso chopereka cha kwa uchimo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma pomwe pali chikhululukiro cha machimo palibenso chopereka cha kwa uchimo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene Mulungu wakhululukira zonsezi, sipafunikanso nsembe yoperekera machimo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo pamene machimo akhululukidwa, sipafunikanso nsembe yoperekedwa chifukwa cha machimowo. |
Ndipo pokhala nacho, abale, chilimbikitso chakulowa m'malo opatulika, ndi mwazi wa Yesu,
Pakadapanda kutero, kodi sakadaleka kuzipereka, chifukwa otumikirawo sakadakhala nacho chikumbumtima cha machimo, popeza adayeretsedwa kamodzi?