3 Yohane 1:15 - Buku Lopatulika Mtendere ukhale nawe. Akupereka moni abwenzi. Upereke moni kwa abwenzi ndi kutchula maina ao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mtendere ukhale nawe. Akupereka moni abwenzi. Upereke moni kwa abwenzi ndi kutchula maina ao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mtendere ukhale nawe. Abwenzi onse akuti moni. Uperekeko moni kwa abwenzi onse mmodzimmodzi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mtendere ukhale nawe. Abwenzi anu kuno akupereka moni. Upereke moni kwa abwenzi onse mmodzimmodzi. |