Koma Yosefe, mwamuna wake, anali wolungama, ndiponso sanafune kunyazitsa iye, nayesa m'mtima kumleka iye m'tseri.
3 Yohane 1:13 - Buku Lopatulika Ndinali nazo zambiri za kukulembera, komatu sindifuna kukulembera ndi kapezi ndi peni; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndinali nazo zambiri za kukulembera, komatu sindifuna kukulembera ndi kapezi ndi peni; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndinali ndi zambiri zoti ndikuuze, koma sindingakonde kuzilemba m'kalata. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndili ndi zambiri zoti ndikulembereni, koma sindikufuna kuzilemba mʼkalata. |
Koma Yosefe, mwamuna wake, anali wolungama, ndiponso sanafune kunyazitsa iye, nayesa m'mtima kumleka iye m'tseri.
Pokhala ndili nazo zambiri zakukulemberani, sindifuna kuchita ndi kalata ndi kapezi; koma ndiyembekeza kudza kwa inu, ndi kulankhula popenyana, kuti chimwemwe chanu chikwanire.