Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okhaokha, muchitanji choposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sachita chomwecho?
2 Yohane 1:13 - Buku Lopatulika Akupereka moni ana a mbale wanu wosankhika. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Akupereka moni ana a mbale wanu wosankhika. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana a mbale wanu wosankhidwa ndi Mulungu akuti moni. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ana a mlongo wanu wosankhidwa ndi Mulungu akupereka moni. |
Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okhaokha, muchitanji choposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sachita chomwecho?
Iye wa ku Babiloni wosankhidwa pamodzi nanu akukupatsani moni; ateronso Marko mwana wanga.